Chipatala cha mpingo wakatolika cha Pirimiti achitseka

Chipatala cha mpingo wakatolika cha Pirimiti mu Boma la Zomba achitseka potsatira kusamvetsetsana komwe kulipo pakati pa ogwira ntchito ndi akuluakulu atatu woona ntchito zapachipatalachi. Malinga ndichikalata chomwe Malawi24 yawona ndipo chasayinidwa ndi wapampando wa bhodi ya chipatala cha Pirimiti Dr Raphael Piringu, izi zachitika potsatira nkumano omwe akuluakulu oyendetsa chipatalachi adali nawo pa 14 […]

The post Chipatala cha mpingo wakatolika cha Pirimiti achitseka appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください