Dr. Triephornia Thomson Mpinganjira, yemwe ndi mkazi wa mpondamatiki Dr. Thomson Mpinganira, wati anthu akadya chakudya cha madzulo ku Bingu International Convention centre (BICC) mu mzinda wa Lilongwe lero pa “bill” yake. Dr. Triephornia, omwenso ndi dziwika bwino pa nkhani za malonda m’dziko muno ngakhalenso mayiko akunja, ati iyi ndi njira imodzi yowathokozera anthu amene […]
The post Triephornia Mpinganjira ankoza mgonero, wokadya ndi anzinake apa Facebook aku Lilongwe: “Tadyako ku President Hotel lero.” appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.