Chipani cha DPP chichenjeza boma: “Osapanga bajeti yokopa anthu pa zisankho, thesani njala, konzani chuma.”

Chipani chotsutsa cha Democratic Progressive (DPP) chachenjeza boma kuti lisakhazikitse ndondomeko ya chuma cha chaka cha 2024 mpaka 2025 yomwe cholinga chake ndi kukopa anthu pomwe dziko lino likukonzekera zisankho. Chenjezoli likubwera pomwe nduna ya zachuma, Simplex Chithyola Banda, akuyembekezeka kupereka ndondomeko ya ya chuma ya 2024/2025 masana ano. Polankhula ndi MIJ Online Mary Navicha, […]

The post Chipani cha DPP chichenjeza boma: “Osapanga bajeti yokopa anthu pa zisankho, thesani njala, konzani chuma.” appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください