Wa polisi wanjatwa kamba koba foni ya mlonda

Wa polisi wa zaka 41 ku Ulongwe m’boma la Machinga ali m’manja mwa apolisi anzake kamba kakuba lamya ya m’manja ya mlonda wina. Malingana ndi lipoti lochokera pa polisi ya Liwonde m’boma la Machinga, omangidwawa ndi Constable Blessings Patrick omwe amagwira ntchito pa polisi yaing’ono ya Ulongwe ndipo akuti achita ukathyaliwu kumayambiliro a sabata ino. […]

The post Wa polisi wanjatwa kamba koba foni ya mlonda appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください