Palibe yemwe afe ndinjala – atelo a Chakwera

Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus McCarthy Chakwera watsimikizira mtundu wa a Malawi kuti palibe ngakhale munthu m’modzi yemwe amwalire chifukwa cha njala yomwe yafika posauzana m’madera ambiri m’dziko muno. A Chakwera amayankhula izi Lachitatu pa 21 February, 2024 pomwe anakaonekera m’nyumba ya malamulo momwe anapita kukayankha mafuso okhudza zinthu zosiyanasiyana makamaka zomwe zikukhudza miyoyo […]

The post Palibe yemwe afe ndinjala – atelo a Chakwera appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください