Chipani cha DPP chikuti a Chakwera ndi munthu wabodza lankunkhuniza

Chipani chotsutsa boma cha DPP chati mtsogoleri wadziko lino Lazarus Chakwera ndimunthu wabodza lankunkhuniza. Izi zadza pamene Chakwera lero anali mnyumba yamalamulo kuyankha mafunso a aphungu. Poyankhula ndi MIJ Online, Mary Navicha mtsogoleri wa DPP mnyumba yamalamulo wati Chakwera zonse zimene wayankhula ndizabodza kamba koti anthu akugona ndinjala komanso ali paumphawi wazaoneni. Navicha wati ngati […]

The post Chipani cha DPP chikuti a Chakwera ndi munthu wabodza lankunkhuniza appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください