Mzibambo wa zaka 47 munzinda wa Lilongwe wathilidwa dzingwe kamba kopezeka ndi ngaka (pangolin), pomwe awiri enaso munzinda omwewu awanjata chifukwa chopezeka ndi nyanga za njovu. Izi ndi malingana ndi ofalitsa nkhani pa polisi ya Lilongwe a Hastings Chigalu omwe azindikira mzibambo opezeka ndi ngaka-yu ngati a Gevinala Makanda pomwe opezeka ndi nyanga za njovu-wa […]
The post Anjatwa kamba kopezeka ndi ngaka, nyanga za njovu appeared first on Malawi 24.