Zoopsa! Azimayi, atsikana akugonana ndi asodzi kuti aziwapatsa milamba, makakana

Atsikana ndi amayi akugonana ndi asodzi pa doko la Bulawayo ku Nsanje n’cholinga choti aziwapatsa milamba ndi makakana. Mkulu woona za ntchito yolimbana ndi edzi a MacKnowledge Tembo komanso woona za ntchito yogawa makondomu m’bomalo a John Maganizo ndiwo atulutsa nkhaniyi patsiku lokumbukira kufunika kwa makondomu pa msika wa Sorgin m’bomalo.   “Atsikana ndi amayi […]

The post Zoopsa! Azimayi, atsikana akugonana ndi asodzi kuti aziwapatsa milamba, makakana appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください