Sitikusinthirani tsiku lobadwa pa chiphaso — NRB

Bungwe lolemba nzika la National Registration Bureau (NRB) lati silisinthila a Malawi omwe akufuna kusinthitsa tsiku lobadwa chifukwa tsiku lobadwa pa chiphaso cha nzika ndilotetezedwa. M’malingana ndi chikalata chomwe bungweli latulutsa pa 19 febuluwale chotsimikidwa ndi mlembi wamkulu wa NRB a Mphatso Sambo, ati bungweli ndilokhudzika ndi kuchuluka kwa anthu amene akusintha tsiku lobadwa pa […]

The post Sitikusinthirani tsiku lobadwa pa chiphaso — NRB appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください