Anthu akudikila kuti adzasankhe ine, atero a shado a ku Zomba Thondwe

Yemwe akufuna kudzayimira chipani cha Democratic Progressive m’dera la Zomba Thondwe pachisankho chakunyumba yamalamulo mi chaka cha 2025 a Dumisani Lindani ati mosakayika konse iwo akudzapambana chisankhocho. A Lindani awuza Malawi24 kuti pakali pano anthu a mdera la Zomba Thondwe akuchikonda chipani cha DPP pamodzi ndi mtsogoleri wachipanichi Professor Peter Muthalika ndipo anthu ambiri ndiwomwe […]

The post Anthu akudikila kuti adzasankhe ine, atero a shado a ku Zomba Thondwe appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください