Mlendo Uladi Mussa akapikisana nawo pa mipando  iwiri ku MCP

Yemwe anali m’modzi mwa akulu akulu ku chipani cha Democratic Progressive  DPP a Uladi Mussa ndipo pakali pano adalowa chipani  cha Malawi Congress (MCP) ati iwo atafatsa kuwelenga malamulo a chipanichi tsopano ali ndi mangongolomela okapikisana nawo pa mipando iwiri ku msonkhano waukulu omwe chipani cha MCP  chipangitse. Poyankhula pa wailesi ya kanema wa Times […]

The post Mlendo Uladi Mussa akapikisana nawo pa mipando  iwiri ku MCP appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください