Ras Chikomeni akuufunabe upulezidenti

Ras Chikomeni David Kadelele Chirwa yemwe amadziwika bwino ndi dzina loti Ras Chikomeni, ati ndi okonzeka kuyimanso ngati m’tsogoleri wa dziko lino pa zisankho za patatu mu 2025. A Chikomeni anali ndi chidwi choyima pa zisankho za 2019, koma izi sizidatheke kamba kosowekera ndalama ya chikole cha zisankho yokwana 2 Million Kwacha, komanso osayinira 19 […]

The post Ras Chikomeni akuufunabe upulezidenti appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください