A Navicha adzudzula ndondomeko yolembetsela voti

Mtsogoleri wa mbali yotsutsa boma wa DPP kunja kwa nyumba ya malamulo a Mary Navicha, ati atengela ku nyumba ya malamulo nkhani yokhudza kalembela wa voti kuti akawunikenso lamulo logwiritsa ntchito chiphaso cha unzika poponya voti kuti zichotsedwe. Polankhula mu msonkhano wa olemba nkhani ku Golden Peakock mu mzinda wa Lilongwe, a Navicha ati apempha […]

The post A Navicha adzudzula ndondomeko yolembetsela voti appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください