Mary Navicha akana kuyankha za SONA mnyumba ya malamulo

Yemwe wangosankhidwa kumene kukhala mtsogoleri wa aphungu otsutsa boma wa chipani cha Democratic Progressive (DPP) m’nyumba  yamalamulo, mayi Mary Navicha akana kulankhulapo m’nyumbayi pa zomwe mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera analankhula pomwe amatsekulira mkumano wa aphungu m’nyumbayi lachisanu. Sipikala wanyumbayi a Catherine Gotani Hara anapeleka mwayi kwa a Navitcha womwe akudziwika m’nyumbayi ngati mtsogoleri wa […]

The post Mary Navicha akana kuyankha za SONA mnyumba ya malamulo appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください