Ubwenzi wa Tay Grin ndi Mutale Mwanza ukuoneka uli pendapenda potsatira uthenga omwe mkaziyu walemba pa tsamba lake la mchezo. Uthengawu ukusonyeza kuti mkaziyu wasweka mtima ndi zomwe bwenzi lake la muchita ngakhale zifukwa zake sanapereke ndipo ukusonyeza kuti ubale wa awiriwa sukuyenda bwino. “Ngakhale titasiyana nthawi ya 11 koloko, dziwa kuti imakati 11:1 koloko […]
The post Mutale watutumutsa gulu ndi uthenga okhudza bwenzi lake Tay Grin appeared first on Malawi 24.