Bungwe la National Aids Commission (NAC) ladandaula ndi kukhudzidwa ndi mauthenga ochuluka komanso malonda okhudzana ndi machiritso a HIV ndi Edzi omwe akumafalitsidwa kwambiri. Chikalata chomwe bungweli lalemba mosogozedwa ndi mkulu wake Betreace Lydia Matanje chati mauthenga komanso malonda abodza, osayenera komanso osokoneza ndioika pa chiopsezo miyoyo ya anthu ambiri omwe ali ndi HIV. Chikalatachi […]
The post Mauthenga ena abodza akuika pa chiopsezo miyoyo ya anthu omwe ali ndi HIV — yatero NAC appeared first on Malawi 24.