Mmodzi wa oyimba nyimbo zauzimu, yemwenso ndi m’busa wa mpingo wa Fountain Gates Assembly, McDonald MlakaMaliro, watsutsa mphekesera zoti iwowa akudwala mwa kayakaya. Kudzera mu program yomwe Times Radio imacheza ndi mbusayu ndi mkazi wawo Benadetta, iwo ati thupi lawo latha chifukwa cha kusala kudya osati nthenda ayi. “Ndakhala ndikusala kuyambira chaka chatha mwezi […]
The post Mlaka asusa mphekesera zoti akudwala mwakayakaya, akuti thupi latha chifukwa chosala kudya appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.