Msika wa Matchansi ku Lilongwe ukosowekera ukhondo

Msika wa Matchansi ku Lilongwe, omwe umadziwika bwino ndi malonda a chakumwa choledzeretsa ndi nyama ya pachiwaya, ukuika pa chiopsezo cha matenda kwa anthu ogula ndi ogulitsa kamba koti dzala lotaila dzinyalala lidayandikana ndi malo ootchela mang’ina komanso bala. Ntchito yosamalira msika imakhala m’manja mwa akuluakulu amene anasankhidwa kupyolera muma voti omwe anthu ochita malonda […]

The post Msika wa Matchansi ku Lilongwe ukosowekera ukhondo appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください