Mtsogoleri wa zipani zotsutsa boma m’nyumba ya malamulo a Kondwani Nankhumwa omwenso ndi phungu wa dera la Mulanje Central, apempha unduna woona za masewero kuti uganizire anthu omwe adasewerapo mpira wa miyendo komanso wa manja m’mbuyomu. A Nankhumwa ati n’zomvetsa chisoni kuona a namandwa ena omwe adasewerapo mpira bwino m’mbuyomu akuvutika kwambiri. Mwachitsanzo a […]
The post Nankhumwa apempha boma liganizire omwe adasewerapo mpira wamiyendo ndi wa manja m’mbuyomu appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.