Inkosi M’mbelwa yaimitsa mafumu asanu

Mfumu yaikulu ya angoni  ku chigawo chakumpoto Inkosi Ya Makosi M’mbelwa Ya Chisanu yayamba yaimitsa kaye mafumu asanu kamba kothandizira kuwononga chilengwe. Mfumu Mbelwa yayankhura izi pa mwambo wobzala mitengo womwe unachitikira pa sukulu ya pulayimale ya Luwelezi m’dera la Inkosi Mabilabo. Mafumu omwe awayimitsawa ndi monga a Chihema, Kasankha, a Chiziyani, a Mchitilare komanso […]

The post Inkosi M’mbelwa yaimitsa mafumu asanu appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください