Katswiri olankhulapo pa nkhani zosiyanasiyana m’dziko muno Latim Matenje wati zomwe zikuchitika Ku nyumba ya malamulo maka ku mbali ya aphungu otsutsa a chipani cha DPP zikuwonetseratu kuti chipanichi sichili chikonzeka kulowa m’boma. Malinga ndi Matenje, wapempha ma bwalo a milandu kuti abwere poyera ndikunena ngati atopa ndi kumva nkhani zokhuza chipani cha DPP kusiyana […]
The post Katswiri akuti DPP siyonkhonzeka kulowa m’boma, kwachuluka zibwana appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.