Aphungu oposa 20 a chipani cha DPP awatulutsa mu nyumba ya malamulo chifukwa anaima kuti alankhule pamene a sipikala anati manja awo ndi omangidwa pa za mtsogoleri wa otsutsa mnyumba ya malamulo ndipo akuona kuti a Kondwani Nankhumwa ndiwo adakali mtsogoleri otsutsa mnyumbayi. Izi zinachitika pamene sipikala wa nyumbayi a Catherine Gotani Hara anawelenga zokambilana […]
The post Aphungu a DPP atulutsidwa mnyumba ya Malamulo appeared first on Malawi 24.