Anthu okhala m’boma la Karonga m’mudzi mwa Mwangosi mfumu yayikulu Kilipula ayamba kuthilira mbewu zawo m’minda yawo pamene kwakhala pafupifupi masabata atatu kopanda mvula. Nelson Manda yemwe ndi ophunzira wapa sukulu ya ukachenjede ya Mzuzu University wauza Malawi24 kuti vuto lakusowa kwa mvula pafupifupi masabata atatu kwapangitsa kuti mbewu ziyambe kuuma m’minda ndipo pofuna kuthana […]
The post Anthu ena ayamba kuchita mothilira mbewu zawo ku Karonga appeared first on Malawi 24.