Bungwe la Evangelical Association of Malawi (EAM) lapempha anthu onse dziko muno kuti pakhale mapemphero apaderadera opemphelera mvula kamba ka ng’amba yomwe yakhudza m’dera ambiri m’dziko muno. Chikalata chomwe wasainira ndi mlembi wamkulu m’bungweli, M’busa Francis Mkandawire, chikumeneza anthu onse dziko muno posatengera chipembedzo kutenga nawo gawo mapempherowa kuti mvuLa iyambeso kugwa moyenera. “Tipempere ma […]
The post Tiyeni tipempherere mvula, latero bungwe la EAM appeared first on Malawi 24.