DPP igwedeza Zomba ndi uthenga wolimbikitsa anthu kuzavota: Khalani ndi chiphaso

Anthu ochuluka akuoneka m’malo momwe akuluakulu ena a chipani cha Democratic Progressive (DPP) akuchititsa misonkhano yomema anthu kuti akhale ndi chiphaso cha unzika. Anthu ochuluka aoneka pa Thondwe, 6 Miles komanso kwa Mpunga m’boma la Zomba. Pakadali pano, m’dipitiwu ukuthamangira mtunda wa kwa Namaraka, komwenso kuli anthu ochuluka. Mwambo wa chipani cha Democratic Progressive Party […]

The post DPP igwedeza Zomba ndi uthenga wolimbikitsa anthu kuzavota: Khalani ndi chiphaso appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください