Prophet Shepherd Bushiri yemwe ndi mtsogoleri wa mpingo wa Enlightened Christian Gathering (ECG) walengeza kuti wayamba pologalamu yogawa chimanga kwa maanja oposa 1 miliyoni omwe akhudzidwa ndi njala mdziko muno. Malingana ndi a Bushiri omwe amayankhula izi kunkhokwe yosungira chimangachi, chimangachi chilipo chokwana 17,000 Metric tons, ndipo ndichandalama zokwana 14 biliyoni Malawi kwacha. Bushiri wapemphanso […]
The post Bushiri wayamba kugawa chimanga cha ndalama zokwana 14 biliyoni appeared first on Malawi 24.