Mai wa zaka 78 waphedwa mu nyumba yake ku Chiradzulu

Apolisi m’boma la Chiradzulu akusakasaka anthu omwe apha  mai wa zaka 78 zakubadwa, Edina Makhumba. Mbandazi zathawaso ndi foni ya manja tamabatani, Nkhuku folo, zofunda, ufa wachimanga olemera 5 kilogalamu komaso ndalama yokwana K20,000. Mneneri wa apolisi ku Chiradzulu, Cosmas Kagulo,  wati izi zachitika m’mudzi wa Iidala m’bomalo. Iwo anapitiliza kunena kuti mwana wa malemuwa  […]

The post Mai wa zaka 78 waphedwa mu nyumba yake ku Chiradzulu appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください