A Mary Navicha omwe chipani cha DPP chawasankha kukhala mtsogoleri wa zipani zotsutsa mnyumbayi ati zomwe Pulezidenti Lazarus Chakwera walankhula palibe chachilendo angobwereza malankhulidwe awo okoma koma kukanika kuchita. Polankhula masanawa ku nyumba ya malamulo a Navicha ati iwo ndiokonzeka kumenyera nkhondo a Malawi powonetsetsa kuti zomwe mtsogoleri-yi walankhula akwaniritse kupanda apo atule pansi udindo […]
The post Navicha adzudzula Chakwera: Palibe chachilendo, angobwereza malankhulidwe appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.