Akulu akulu a boma la Machinga ati mitengo yomwe inali pa malo okwana mahekitala okwana 50 mu nkhalango zosiyasiyana yadulidwa mu zaka wiri zapitazo. Wapampando mu khosolo ya Machinga, Cydreck Stande, anati mchitidwewu ukupitilila kamba kakuchepa kwa chitetezo mu nkhalangozi zimene zikupereka mpata kwa anthu ozungulila kuti adzilowa ndi kudula mitengo kuti adziwotchera makala zomwe […]
The post Adandaula ndi mchitidwe odula mitengo mwa chisawawa ku Machinga appeared first on Malawi 24.