Bungwe la Malawi Communications Regulatory Authority (MACRA) yalamula kuti nyumba zowulutsa mawu zomwe zimanenerera mpira pomwe zikuonera mmakanena akunja kapena a m’dziko muno zikuyenera kupereka umboni kuti zili ndi chilolezo chochita izi pasanathe masiku asanu ndi awiri kuchokera pa 5 February chaka chino. Malingana ndi kalata yomwe bungweli latulutsa ndipo yasainidwa ndi mkulu wa bungweli […]
The post MACRA yalamula mawailesi omwe amanenelera mpira uku wakunja kuti azikhala ndi chilolezo appeared first on Malawi 24.