DPP ikuyenera kudekha pochotsa Nankhumwa pa mpando wa mtsogoleri otsutsa ku parliament, atero katswiri

M’modzi mwa oyankhula pankhani zosiyanasiyana, Wonderful Mkhutche walangiza chipani chotsutsa boma cha DPP kuti chidekhe pa chiganizo chake chochotsa Kondwani Nankhumwa ngati mtsogoleri wa aphungu otsutsa boma ku nyumba ya malamulo. Sabata latha, chipanichi chinasankha George Chaponda ngati mtsogoleri watsopano wambali yotsutsa munyumbayi kulowa m’malo mwa Nankhumwa.   Koma pakadali pano, bwalo lamilandu laletsa kuchotsedwa […]

The post DPP ikuyenera kudekha pochotsa Nankhumwa pa mpando wa mtsogoleri otsutsa ku parliament, atero katswiri appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください