Namondwe wa Freddy komanso mchitidwe okuba zichitsulo cha njanji ndi zina mwa zomwe zachedwetsa ntchito yokonzaso njanji ya makilomita 72 ya Limbe-Sandama. Nduna yoyang’anira mayendwe komaso ntchito, Jocobo Hara, wati pakadali pano sizikudziwika nthawi yeniyeni imene ntchito yi idzamalizidwe chifukwa contilakitala sakugwira ntchitoyi. A Hara anauluraso kuti namondwe anaononga milatho yambiri imene imalumikiza njanjiyi komaso […]
The post Mchitidwe wa kadzanja ukuchedwetsa ntchito yokonzaso njanji ya Limbe-Sandama appeared first on Malawi 24.