A Malawi ambiri omwe tayankhula nawo aikila kumbuyo ganizo lomwe anthu wena akhala akunena kuti pakhale lamulo lomwe cholinga chake ndi kuonenetsa kuti pakhale malire a zaka zomwe munthu akuyenera akhale nazo kuti aime pa masankho a utsogoleri wa dziko lino. Izi zikuchitika ngakhale zipani dzotsitsa boma zakhala zikukana ganizoli potengera kutimtsogoleri wawo kuchipani […]
The post A Malawi aikila kumbuyo ganizo lopanga lamulo lomwe lidziletsa nkhalamba kuima pa chisankho appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.