Apolisi m’boma la thyolo akusaka bambo Nyozani Phiri a zaka makumi atatu zakubadwa powaganizira kuti ndi amene apha mkazi wawo wachinayi, Lucy San wa zaka makumi atatu zakubadwa. Wachiwiri kwa mneneri wa apolisi m’boma la thyolo, sagenti Rebecca Kashoti, wati bambo Phiri anali ndi akazi anai ndipo mu usiku wathawu iwo anali pa mikangano ndi […]
The post Asakidwa ndi apolisi kamba ka kokupha mkazi wawo appeared first on Malawi 24.