Salary K52000 thumba lachimanga K50 000? Adabwa ogwira ntchito zapakhomo pokana zomwe boma lakhazikitsa

Ogwira ntchito za pakhomo komanso m’mashopu ati ndi chitonzo chachikulu chomwe boma lapanga chifukwa iwowa amagwira ntchito yambiri ndipo ati n’zomvetsa chisoni kuona boma likufananiza malipiro awo ndi thumba limodzi la chimanga. Izi ogwira nthitowa anena mu mzinda wa Lilongwe  pomwe anachititsa msonkhano wa atolankhani poonetsa kusakondwa ndi ganizo la boma pa malipiro a anthu […]

The post Salary K52000 thumba lachimanga K50 000? Adabwa ogwira ntchito zapakhomo pokana zomwe boma lakhazikitsa appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください