Pamene nyumba ya malamulo ya dziko lino yatsala ndi masiku wochepa kuti iyambe zokambirana zake, pali kuthekera kuti zokambirana mnyumbayi zitha kukhala zovuta. Izi zili chomwechi kutsatira chiganizo chomwe Sipikala wa nyumbayi a Catherine Gotani Hara molangizidwa ndi mkulu wa zamalamulo ku boma a Thabo Nyirenda apanga posavomereza kusankhidwa kwa a George Chaponda ngati mtsogoleri […]
The post Zokambirana zikuyembekezeka kukavuta ku nyumba ya malamulo appeared first on Malawi 24.