Katswiri osewera ku tsogolo, Clement Nyondo, wasintha thabwa tsopano pamene walowa timu ya Mighty Wanderers potsatira kuchoka ku timu ya Dedza Dynamos. Nyondo, amene ali ndi zaka 23 ndipo anatenga mphoto ya katakwe omwetsa zigoli zambiri ( Golden Boot Award) mu TNM Super League ndi zigoli 16 chaka chatha, wasayina mgwirizano wa zaka zitatu ku […]
The post Clement Nyondo wafika ku Wanderers, wasayina mgwirizano wa zaka zitatu appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.