DoDMA yati makhonsolo 20 akhudzidwa ndi ngozi zogwa mwadzidzidzi chiyambileni nyengo ya mvula

Nthambi Yoona za Ngozi zogwa mwadzidzidzi (DoDMA) yomwe ili mu Ofesi ya Mtsogoleri wa Dziko Lino ndi Nduna, yati kuyambila m’mwezi wa October chaka chatha kufika mwezi uno, makhonsolo makumi awiri (20) m’dziko muno akhudzidwa ndi ngozi zogwa mwadzidzi. Izi zadziwika pamene nthambiyi imapeleka tsatanetsatane wa ngozi zogwa mwadzidzi ndi ntchito yopereka thandizo ku maanja […]

The post DoDMA yati makhonsolo 20 akhudzidwa ndi ngozi zogwa mwadzidzidzi chiyambileni nyengo ya mvula appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください