Nduna yoona za malamulo, a Titus Mvalo yati mtsogoleri wadziko lino a Lazarus Chakwera wakhululukira akaidi oposa 8,000 kuchoka m’chaka cha 2020. Iwo ati kukhulukira akaidiku ndi njira imodzi yochepetsera kuthithikana ndi mu ndende za dziko lino. A Mvalo, omwe ndi wapampando wa komiti yomwe imaunikira nkhani zokhulukira akaidi, ayankhula izi atatsogolera komitiyi, kuona zomwe […]
The post Mzaka zitatu zapitazi Chakwera wakhululukira akaidi oposa 8000 appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.