Chiyamba kale pa maimbidwe Lucius Banda watayira ka mtengo oyimba wamakono, Patience Namadingo, poyankhula zakupsa posachedwapa koma wadzudzula anthu mdziko muno kuti asiye mchitidwe oyika oyimba pa mpikisano. Izi zili mu uthenga omwe Banda wayika pa tsamba lake la fesibuku Lachitatu pa 31 January, 2024 momwe amayamikira mfundo zokhwima komaso zogwira ntima zomwe Namadingo anayankhula […]
The post Watiyankhulira bwino: A Malawi lekani kuika oyimba pa mpikisano – Lucius Banda watayira ka mtengo Namadingo appeared first on Malawi 24.