Tsopano nthambi yoona zanyengo ndi kusintha kwa nyengo yati kuyambira mawa pa 1 February mvula ikhala ikugwa m’dziko muno patapita pafupifupi sabata ndi masiku kopanda mvula maka m’madera am’chigawo chapakati komanso kum’mwera kwa dziko lino. Malingana ndi mneneri ku nthambiyi a Yobu Kachiwanda, ati mvula ikhala mwezi onse uno wa February. Kachiwanda wati ngakhale kuti […]
The post Mvula ikhala ikugwa kuyambira mawa, atero azanyengo appeared first on Malawi 24.