Dziko la Israel lati likufuna a Malawi okwana 100,000 kuti akagwire ntchito zosiyanasiyana ku Israel. Izi zayankhulidwa lero pamene nduna ya zachuma mu dziko la Israel, Nir Barakt, anali ndi mkumano ndi mlembi wamkulu mu unduwa wa zachuma mu dziko lino Dr Betchani Tchereni. A Barakt atsimikizira kuti mwai wa ntchito ulipo wambiri dziko la […]
The post Dziko la Israel likufuna a Malawi okwana 100,000 appeared first on Malawi 24.