Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera apempha a Malawi kuti akondane pogawana ka chakudya kochepa kamene anthu ali nako mu nyengo ya njala ino yomwe imakhala miyezi yovuta kawirikawiri. Poyankhula lero Ku Dowa pa bwalo la Andrew Murray ku Mvera atayendera Nyumba zomwe zikumangidwa za asilikali a nkhondo ku Mvera Support Batallion mu ulendo […]
The post Ka chakudya tili nakoko tigawane, atero a Chakwera appeared first on Malawi 24.