Pelekani molowa manja: Sinodi ya Blantyre pansi pa mpingo wa Church of Central Africa Presbyterian (CCAP) yakhazikitsa ntchito yobweza ngongole ya ndalama zokwana 2 biliyoni kwacha ndipo yagwada kupempha akhilisitu ake kupeleka 10,000 kwacha aliyese. Sinodiyi Lamulungu pa 28 January, 2024, yatulutsa kalata yokhazikitsa ntchito yobweza ngongole ya ndalama zokwana 2 biliyoni kwacha yomwe mpingowu […]
The post Tibhebhetseni 10 pini – Blantyre Sinodi yapempha membala aliyese appeared first on Malawi 24.