Chaka chamawa ndilipo pa ballot paper – Nankhumwa

Inu nonse amene mukutangwa ndikumalemba kuti APM my vote, kapena Chakwera my vote, dziwani kuti mpikisano opita ku state house ukupita kotenthera. Nawo a Kondwani Nankhumwa amene anapitikitsidwa ku chipani cha DPP alonjeza kuti muwaona akupikitsana nawo pa masankhowa. Polankhula kwa anthu amene akuti ndi owatsatira mu mzinda wa Ndirande, a Nankhumwa ati iwo adachotsedwa […]

The post Chaka chamawa ndilipo pa ballot paper – Nankhumwa appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください