…Lombwe akuti nzakeyo anakhomera ku dowa “Lu-Lo my vote”: Kuli kusambwadzana za mkabudula uku pomwe mtsutso wa ubwino wokhala ndi digili kapena kungokhala ndi chilembwe basi, wafika pa mwana wakana phala pakati pa oyimba Dan Lu ndi Kabol Lombwe ndipo nkhaniyi yatsikira ku ma Area. Nkhaniyi inayamba pa 19 January, 2024 pomwe oyimba Dan Lufani […]
The post Digili, kapena mteleshede? Dan Lu, Lombwe akusambulana uku appeared first on Malawi 24.