Mnyamata wagwililira mbuzi ku Ntchisi

Zina inu mkumafunsa kuti kodi anyamata oshanganipawa akukanika kufunsira mbeta? Zina ndithu ukamva ngati kutulo. Mnyamata wazaka 26 ku Ntchisi ali mchitokosi cha apolisi kamba koti amachita zadama ndi mbuzi. Malingana ndi mneneri wa apolisi m’bomali a Sub Inspector Salomy Zgambo, mnyamatayu dzina lake ndi Vincent Mwale ndipo adachita zamalawulozi la chinayi pa 25 January […]

The post Mnyamata wagwililira mbuzi ku Ntchisi appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください