Boma kudzera mwa nduna yoona zamagetsi mdziko muno a Ibrahim matola, lalonjeza kuti lithandiza nyamata uja wakonza magetsi oyendera madzi ndi mpweya ku Dowa kufikira masomphenya ake oyika magetsi pa sukulu ya Kongwe 2 komanso nyumba za m’mudzi mwake atakwanilitsidwa. Nduna yoona za magetsi mdziko muno a Ibrahim Matola ndi omwe ayankhula izi lero la […]
The post Boma lati ligwira ntchito limodzi ndi mnyamata wakonza magetsi ku Dowa appeared first on Malawi 24.