Akathyali atatu akhwidzingidwa ndi apolisi ku Lilongwe kaamba kowaganizira kuti adayendetsa champeni (kuba) lamya za m’manja za anafedwa pamaliro dzulo m’mudzi wa Kamganga kwa mfumu yaikulu Mavwere m’boma la Mchinji. Nkhani yonse ikuti akathyali atatuwa omwe mayina awo ndi a Steven Mofolo azaka 31, a Andrew Manase azaka 28 komanso a Innocent Phiri azaka 33, […]
The post Akathyali atatu awanjata kamba koyendetsa champeni lamya za anamfedwa pamaliro appeared first on Malawi 24.
Moni Malawi 