Apolisi ayamba kumanga omwe anatchingira nsewu Chakwera ku Blantyre

Malipoti osatsimikizika akusonyesa kuti apolisi munzinda wa Blantyre amanga anthu awiri powaganizira kuti anali nawo mu gulu la anamalira omwe anatchingira nsewu mdipiti wa galimoto za mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera pa mphambano ya HHI ku Blantyre, koma ofalitsa nkhani za apolisi mdziko muno wati atitsimikizirabe ngati mphekeserazi zili zoona. Lachisanu lapitali, kunali […]

The post Apolisi ayamba kumanga omwe anatchingira nsewu Chakwera ku Blantyre appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください